Mateyu 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Filipo ndi Batolomeyo,+ Tomasi+ ndi Mateyu+ wokhometsa msonkho, Yakobo mwana wa Alifeyo,+ Tadeyo, Luka 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anasankha Simoni, amenenso anam’patsa dzina lakuti Petulo,+ ndi m’bale wake Andireya. Anasankhanso Yakobo ndi Yohane,+ Filipo+ ndi Batolomeyo,
14 Iye anasankha Simoni, amenenso anam’patsa dzina lakuti Petulo,+ ndi m’bale wake Andireya. Anasankhanso Yakobo ndi Yohane,+ Filipo+ ndi Batolomeyo,