Machitidwe 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Munthu uyu anagwidwa ndi Ayuda ndipo anali pafupi kumupha. Koma ine ndinafika mwadzidzidzi ndi gulu la asilikali n’kumulanditsa,+ chifukwa ndinamva kuti iyeyu ndi Mroma.+
27 Munthu uyu anagwidwa ndi Ayuda ndipo anali pafupi kumupha. Koma ine ndinafika mwadzidzidzi ndi gulu la asilikali n’kumulanditsa,+ chifukwa ndinamva kuti iyeyu ndi Mroma.+