Luka 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma khamu lonse linafuulira pamodzi kuti: “Ameneyu muthane naye basi,+ koma ife mutimasulire Baraba!”+ Yohane 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma iwo anafuula kuti: “Muthane naye! Muthane naye! M’pachikeni!” Pilato anawafunsa kuti: “Kodi ndipachike mfumu yanu?” Ansembe aakulu anayankha kuti: “Tilibe mfumu ina koma Kaisara.”+ Machitidwe 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iwo anali kumumvetsera mpaka pa mawu amenewa. Kenako anafuula kuti: “Munthu ameneyu asapezekenso padziko lapansi, chifukwa sakuyenera kukhala ndi moyo!”+
18 Koma khamu lonse linafuulira pamodzi kuti: “Ameneyu muthane naye basi,+ koma ife mutimasulire Baraba!”+
15 Koma iwo anafuula kuti: “Muthane naye! Muthane naye! M’pachikeni!” Pilato anawafunsa kuti: “Kodi ndipachike mfumu yanu?” Ansembe aakulu anayankha kuti: “Tilibe mfumu ina koma Kaisara.”+
22 Iwo anali kumumvetsera mpaka pa mawu amenewa. Kenako anafuula kuti: “Munthu ameneyu asapezekenso padziko lapansi, chifukwa sakuyenera kukhala ndi moyo!”+