Machitidwe 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo iwowa sanandipezepo m’kachisi+ ndikutsutsana ndi wina aliyense, ngakhale kuyambitsa chipolowe+ m’masunagoge kapena pena paliponse mumzindawu. Machitidwe 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Paulo podziteteza anati: “Ine sindinachimwire Chilamulo cha Ayuda, kapena kachisi,+ kapena Kaisara.”+
12 Ndipo iwowa sanandipezepo m’kachisi+ ndikutsutsana ndi wina aliyense, ngakhale kuyambitsa chipolowe+ m’masunagoge kapena pena paliponse mumzindawu.
8 Koma Paulo podziteteza anati: “Ine sindinachimwire Chilamulo cha Ayuda, kapena kachisi,+ kapena Kaisara.”+