1 Akorinto 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Palibe wolamulira+ ndi mmodzi yemwe wa nthawi* ino amene anadziwa+ nzeru imeneyi, chifukwa ngati anali kuidziwa sakanapachika+ Ambuye waulemereroyo.
8 Palibe wolamulira+ ndi mmodzi yemwe wa nthawi* ino amene anadziwa+ nzeru imeneyi, chifukwa ngati anali kuidziwa sakanapachika+ Ambuye waulemereroyo.