Yohane 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komabe onse amene anamulandira,+ anawapatsa mphamvu zokhala ana a Mulungu,+ chifukwa amenewa anakhulupirira m’dzina lake.+ Yohane 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yesu anayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuza, Munthu sangathe kulowa mu ufumu wa Mulungu atapanda kubadwa mwa madzi+ ndi mzimu.+ Yohane 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mphepo+ imawombera kumene ikufuna, ndipo munthu amamva mkokomo wake, koma sadziwa kumene ikuchokera ndi kumene ikupita. N’chimodzimodzinso aliyense wobadwa mwa mzimu.”+ Aheberi 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti onse, woyeretsayo ndi amene akuyeretsedwawo,+ amachokera kwa mmodzi.+ Pa chifukwa chimenechi, iye sachita manyazi kuwatcha “abale,”+
12 Komabe onse amene anamulandira,+ anawapatsa mphamvu zokhala ana a Mulungu,+ chifukwa amenewa anakhulupirira m’dzina lake.+
5 Yesu anayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuza, Munthu sangathe kulowa mu ufumu wa Mulungu atapanda kubadwa mwa madzi+ ndi mzimu.+
8 Mphepo+ imawombera kumene ikufuna, ndipo munthu amamva mkokomo wake, koma sadziwa kumene ikuchokera ndi kumene ikupita. N’chimodzimodzinso aliyense wobadwa mwa mzimu.”+
11 Pakuti onse, woyeretsayo ndi amene akuyeretsedwawo,+ amachokera kwa mmodzi.+ Pa chifukwa chimenechi, iye sachita manyazi kuwatcha “abale,”+