Machitidwe 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Ayuda anafika kuchokera ku Antiokeya ndi ku Ikoniyo ndipo anakopa anthuwo.+ Choncho anaponya Paulo miyala ndi kumukokera kunja kwa mzindawo, poganiza kuti wafa.+ 2 Akorinto 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Timazunzidwa, koma osati mochita kusowa kolowera.+ Timagwetsedwa pansi,+ koma sitiwonongedwa.+
19 Ndiyeno Ayuda anafika kuchokera ku Antiokeya ndi ku Ikoniyo ndipo anakopa anthuwo.+ Choncho anaponya Paulo miyala ndi kumukokera kunja kwa mzindawo, poganiza kuti wafa.+