2 Akorinto 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ngati osadziwika koma odziwika bwino,+ ngati oti tikufa koma tikukhalabe ndi moyo,+ ngati olangidwa+ koma osakaphedwa,+ 2 Akorinto 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Katatu anandimenya ndi ndodo.+ Kamodzi anandiponya miyala.+ Chombo chinandiswekerapo katatu.+ Kamodzi ndinakhala pamadzi akuya usiku ndi usana wonse. 2 Timoteyo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ukudziwanso mazunzo ndi masautso amene ndinakumana nawo ku Antiokeya,+ ku Ikoniyo,+ ndi ku Lusitara.+ Komabe, Ambuye anandipulumutsa m’mazunzo onsewa.+
9 ngati osadziwika koma odziwika bwino,+ ngati oti tikufa koma tikukhalabe ndi moyo,+ ngati olangidwa+ koma osakaphedwa,+
25 Katatu anandimenya ndi ndodo.+ Kamodzi anandiponya miyala.+ Chombo chinandiswekerapo katatu.+ Kamodzi ndinakhala pamadzi akuya usiku ndi usana wonse.
11 Ukudziwanso mazunzo ndi masautso amene ndinakumana nawo ku Antiokeya,+ ku Ikoniyo,+ ndi ku Lusitara.+ Komabe, Ambuye anandipulumutsa m’mazunzo onsewa.+