Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Popeza Chilamulo chinaperekedwa kudzera mwa Mose,+ kukoma mtima kwakukulu+ komanso choonadi+ zinakhalako kudzera mwa Yesu Khristu.

  • Aroma 3:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndiponso, kuyesedwa olungama chifukwa cha kukoma mtima kwake kwakukulu+ kumene wakusonyeza, powamasula ndi dipo+ lolipiridwa ndi Khristu Yesu, kuli ngati mphatso yaulere.+

  • Aroma 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma mmene zilili ndi mphatsoyi si mmene zinalili ndi uchimowo. Popeza ngati mwa uchimo wa munthu mmodzi ambiri anafa, kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu ndiponso mphatso yake yaulere zinasefukira kwa anthu ambiri.+ Mphatso yaulere imeneyi inaperekedwa limodzi ndi kukoma mtima kwakukulu kudzera mwa munthu mmodzi,+ Yesu Khristu.

  • Aefeso 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndinakhala mtumiki+ wa zimenezi mogwirizana ndi mphatso yaulere ya kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, kumene ndinapatsidwa mogwirizana ndi mmene mphamvu yake imagwirira ntchito.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena