Salimo 110:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova walumbira+ (ndipo sadzasintha maganizo). Iye wati:+“Iwe ndiwe wansembe mpaka kalekale,+Monga mwa unsembe wa Melekizedeki!”+ Aheberi 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Malemba amachitira umboni kuti: “Iwe ndiwe wansembe mpaka muyaya monga mwa unsembe wa Melekizedeki.”+
4 Yehova walumbira+ (ndipo sadzasintha maganizo). Iye wati:+“Iwe ndiwe wansembe mpaka kalekale,+Monga mwa unsembe wa Melekizedeki!”+
17 Pakuti Malemba amachitira umboni kuti: “Iwe ndiwe wansembe mpaka muyaya monga mwa unsembe wa Melekizedeki.”+