Mateyu 10:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Amene walandira mneneri chifukwa ndi mneneri adzalandira mphoto yofanana ndi imene mneneri amalandira,+ ndipo amene walandira munthu wolungama chifukwa ndi wolungama adzalandira mphoto yofanana ndi imene munthu wolungama amalandira.+ Mateyu 25:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pakuti ine ndinamva njala koma inu munandipatsa chakudya.+ Ndinamva ludzu koma inu munandipatsa chakumwa. Ndinali mlendo koma inu munandilandira bwino.+ Machitidwe 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ndipo Yasoni anawalandira bwino. Anthu onsewa akuchita zotsutsana ndi malamulo+ a Kaisara. Akunena kuti eti kulinso mfumu ina+ dzina lake Yesu.” Filimoni 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komanso, ukonzeretu malo anga ogona,+ pakuti ndili ndi chikhulupiriro chakuti chifukwa cha mapemphero+ anu, ndimasulidwa+ kuti ndidzakutumikireni. 1 Petulo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muzicherezana popanda kudandaula.+
41 Amene walandira mneneri chifukwa ndi mneneri adzalandira mphoto yofanana ndi imene mneneri amalandira,+ ndipo amene walandira munthu wolungama chifukwa ndi wolungama adzalandira mphoto yofanana ndi imene munthu wolungama amalandira.+
35 Pakuti ine ndinamva njala koma inu munandipatsa chakudya.+ Ndinamva ludzu koma inu munandipatsa chakumwa. Ndinali mlendo koma inu munandilandira bwino.+
7 ndipo Yasoni anawalandira bwino. Anthu onsewa akuchita zotsutsana ndi malamulo+ a Kaisara. Akunena kuti eti kulinso mfumu ina+ dzina lake Yesu.”
22 Komanso, ukonzeretu malo anga ogona,+ pakuti ndili ndi chikhulupiriro chakuti chifukwa cha mapemphero+ anu, ndimasulidwa+ kuti ndidzakutumikireni.