Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 30:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Malo otchedwa Tofeti*+ owonongerako Asuri akonzedwa kale. Malowo akonzedweranso mfumu yawo.+ Malo amene iye wakonzawo ndi ozama ndipo kuli moto waukulu ndi nkhuni zambiri. Mpweya wa Yehova ukuyatsa malowo ngati mtsinje wa sulufule.+

  • Mateyu 10:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Musachite mantha+ ndi amene amapha thupi koma sangaphe moyo, m’malomwake, muziopa iye+ amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe m’Gehena.*+

  • Chivumbulutso 19:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma chilombocho+ chinagwidwa limodzi ndi mneneri+ wonyenga uja, amene anachita zizindikiro+ pamaso pa chilombocho. Zizindikiro zimenezi anasocheretsa nazo olandira chizindikiro+ cha chilombo ndi olambira chifaniziro chake.+ Adakali amoyo, onse awiri anaponyedwa m’nyanja ya moto yoyaka ndi sulufule.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena