Chivumbulutso 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Ine ndikuchitira umboni kwa aliyense wakumva mawu a ulosi wa mumpukutuwu, kuti: Wina akawonjezera+ pa zimenezi, Mulungu adzamuwonjezera miliri+ yolembedwa mumpukutuwu.
18 “Ine ndikuchitira umboni kwa aliyense wakumva mawu a ulosi wa mumpukutuwu, kuti: Wina akawonjezera+ pa zimenezi, Mulungu adzamuwonjezera miliri+ yolembedwa mumpukutuwu.