Danieli 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anandiuza kuti: “Ine ndikudziwitsa zimene zidzachitike kumapeto kwa nthawi yopereka chiweruzo, chifukwa chakuti masomphenyawo adzakwaniritsidwa pa nthawi yoikidwiratu ya mapeto.+ Chivumbulutso 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anandiuzanso kuti: “Usatsekere mawu a ulosi a mumpukutu uwu, pakuti nthawi yoikidwiratu yayandikira.+
19 Kenako anandiuza kuti: “Ine ndikudziwitsa zimene zidzachitike kumapeto kwa nthawi yopereka chiweruzo, chifukwa chakuti masomphenyawo adzakwaniritsidwa pa nthawi yoikidwiratu ya mapeto.+
10 Anandiuzanso kuti: “Usatsekere mawu a ulosi a mumpukutu uwu, pakuti nthawi yoikidwiratu yayandikira.+