Chivumbulutso 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kuzungulira mpando wachifumuwo, panalinso mipando yachifumu yokwanira 24. Pamipando yachifumuyo,+ ndinaona patakhala akulu+ 24+ ovala malaya akunja oyera,+ ndi zisoti zachifumu+ zagolide pamitu pawo.
4 Kuzungulira mpando wachifumuwo, panalinso mipando yachifumu yokwanira 24. Pamipando yachifumuyo,+ ndinaona patakhala akulu+ 24+ ovala malaya akunja oyera,+ ndi zisoti zachifumu+ zagolide pamitu pawo.