Yohane 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa idzafika nthawi pamene onse ali m’manda achikumbutso+ adzamva mawu ake Machitidwe 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo ine ndili ndi chiyembekezo+ mwa Mulungu, chimenenso anthu awa ali nacho, kuti kudzakhala kuuka+ kwa olungama+ ndi osalungama omwe.+ Aefeso 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiponso, Mulungu anapangitsa inuyo kukhala amoyo pamene munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu ndi machimo anu.+
28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa idzafika nthawi pamene onse ali m’manda achikumbutso+ adzamva mawu ake
15 Ndipo ine ndili ndi chiyembekezo+ mwa Mulungu, chimenenso anthu awa ali nacho, kuti kudzakhala kuuka+ kwa olungama+ ndi osalungama omwe.+
2 Ndiponso, Mulungu anapangitsa inuyo kukhala amoyo pamene munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu ndi machimo anu.+