Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 29:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Anakhalanso woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna, ndipo anati: “Tsopano nditamanda Yehova.” Choncho Leya anamupatsa mwanayo dzina lakuti Yuda.*+ Atabereka mwana ameneyu, anasiya kaye kubereka.

  • Genesis 46:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ana a Yuda+ anali Ere, Onani, Shela,+ Perezi+ ndi Zera.+ Koma Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+

      Ana a Perezi anali Hezironi ndi Hamuli.+

  • Numeri 2:3, 4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Amene azimanga msasa wawo kumʼmawa kotulukira dzuwa ndi gulu la mafuko atatu la Yuda ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Yuda ndi Naasoni,+ mwana wa Aminadabu. 4 Asilikali ake amene analembedwa mayina alipo 74,600.+

  • 1 Mbiri 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ngakhale kuti Yuda+ anali wamphamvu pakati pa azichimwene ake ndiponso kubanja lake kunachokera wodzakhala mtsogoleri,+ udindo wa woyamba kubadwa unali wa Yosefe.

  • Mateyu 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Abulahamu anabereka Isaki.+

      Isaki anabereka Yakobo.+

      Yakobo anabereka Yuda+ ndi azichimwene ake.

  • Aheberi 7:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tonse tikudziwa kuti Ambuye wathu anachokera ku fuko la Yuda+ koma Mose sananenepo kuti ansembe adzachokera mu fuko limeneli.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena