Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Nawonso anthu a ku Gibiyoni+ anamva zimene Yoswa anachita ku Yeriko+ ndi ku Ai.+

  • Yoswa 9:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Koma pa tsikuli, Yoswa anawalamula kuti azitunga madzi ndi kutola nkhuni za Aisiraeli onse+ ndiponso zapaguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.+

  • 1 Mbiri 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Oyamba kubwerera nʼkukakhala kucholowa chawo mʼmizinda yawo anali Aisiraeli ena, ansembe, Alevi ndi atumiki apakachisi.*+

  • Ezara 2:43-54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Atumiki apakachisi:*+ Ana a Ziha, ana a Hasufa, ana a Tabaoti, 44 ana a Kerosi, ana a Siyaha, ana a Padoni, 45 ana a Lebana, ana a Hagaba, ana a Akubu, 46 ana a Hagabu, ana a Salimai, ana a Hanani, 47 ana a Gideli, ana a Gahara, ana a Reyaya, 48 ana a Rezini, ana a Nekoda, ana a Gazamu, 49 ana a Uziza, ana a Paseya, ana a Besai, 50 ana a Asena, ana a Meyuni, ana a Nefusimu, 51 ana a Bakibuki, ana a Hakufa, ana a Harihuri, 52 ana a Baziluti, ana a Mehida, ana a Harisa, 53 ana a Barikosi, ana a Sisera, ana a Tema, 54 ana a Neziya ndi ana a Hatifa.

  • Ezara 2:58
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 58 Atumiki onse apakachisi* pamodzi ndi ana a atumiki a Solomo analipo 392.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena