Yoswa 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nawonso anthu a ku Gibiyoni+ anamva zimene Yoswa anachita ku Yeriko+ ndi ku Ai.+ Yoswa 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma pa tsikuli, Yoswa anawalamula kuti azitunga madzi ndi kutola nkhuni za Aisiraeli onse+ ndiponso zapaguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.+ Ezara 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako ndinawalamula kuti apite kwa Ido yemwe anali mtsogoleri pamalo otchedwa Kasifiya. Ndinawauza mawu oti akauze Ido ndi abale ake, atumiki apakachisi* omwe anali ku Kasifiyako kuti atibweretsere atumiki apanyumba ya Mulungu wathu.
27 Koma pa tsikuli, Yoswa anawalamula kuti azitunga madzi ndi kutola nkhuni za Aisiraeli onse+ ndiponso zapaguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.+
17 Kenako ndinawalamula kuti apite kwa Ido yemwe anali mtsogoleri pamalo otchedwa Kasifiya. Ndinawauza mawu oti akauze Ido ndi abale ake, atumiki apakachisi* omwe anali ku Kasifiyako kuti atibweretsere atumiki apanyumba ya Mulungu wathu.