Salimo 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu amene amaopa Yehova ndi amene amakhala naye pa ubwenzi wolimba,+Ndipo amawadziwitsa pangano lake.+ Miyambo 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chifukwa Yehova amanyansidwa ndi munthu wachiphamaso,+Koma anthu owongoka mtima amakhala nawo pa ubwenzi wolimba.+
14 Anthu amene amaopa Yehova ndi amene amakhala naye pa ubwenzi wolimba,+Ndipo amawadziwitsa pangano lake.+
32 Chifukwa Yehova amanyansidwa ndi munthu wachiphamaso,+Koma anthu owongoka mtima amakhala nawo pa ubwenzi wolimba.+