Salimo 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzakhala malo otetezeka* komwe anthu oponderezedwa angathawireko,+Malo otetezeka othawirako pa nthawi ya mavuto.+ Yesaya 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Yehova, tikomereni mtima.+ Chiyembekezo chathu chili pa inu. Tilimbitseni ndi dzanja lanu+ mʼmawa uliwonse.Mukhale chipulumutso chathu pa nthawi yamavuto.+
9 Yehova adzakhala malo otetezeka* komwe anthu oponderezedwa angathawireko,+Malo otetezeka othawirako pa nthawi ya mavuto.+
2 Inu Yehova, tikomereni mtima.+ Chiyembekezo chathu chili pa inu. Tilimbitseni ndi dzanja lanu+ mʼmawa uliwonse.Mukhale chipulumutso chathu pa nthawi yamavuto.+