Yobu 14:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,Amakhala ndi moyo waufupi+ komanso wodzaza ndi mavuto.+ 2 Amaphuka ngati duwa kenako nʼkufota.+Amathawa ngati mthunzi ndipo saonekanso.+ Salimo 102:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtima wanga wakhala ngati udzu umene wawauka nʼkuuma,+Chifukwa sindikulakalaka kudya chakudya.
14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,Amakhala ndi moyo waufupi+ komanso wodzaza ndi mavuto.+ 2 Amaphuka ngati duwa kenako nʼkufota.+Amathawa ngati mthunzi ndipo saonekanso.+