1 Mafumu 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mikaya anati: “Choncho imvani mawu a Yehova: Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu+ ndipo gulu lonse lakumwamba linaimirira kumanja ndi kumanzere kwake.+ Salimo 148:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mutamandeni, inu angelo ake onse.+ Mutamandeni, inu magulu ake onse akumwamba.+ Luka 2:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwadzidzidzi, panaoneka gulu lalikulu lakumwamba lili limodzi ndi mngeloyo+ ndipo linkatamanda Mulungu kuti: 14 “Ulemerero kwa Mulungu kumwambamwamba, ndipo padziko lapansi pano mtendere pakati pa anthu amene iye amasangalala nawo.”
19 Mikaya anati: “Choncho imvani mawu a Yehova: Ndinaona Yehova atakhala pampando wake wachifumu+ ndipo gulu lonse lakumwamba linaimirira kumanja ndi kumanzere kwake.+
13 Mwadzidzidzi, panaoneka gulu lalikulu lakumwamba lili limodzi ndi mngeloyo+ ndipo linkatamanda Mulungu kuti: 14 “Ulemerero kwa Mulungu kumwambamwamba, ndipo padziko lapansi pano mtendere pakati pa anthu amene iye amasangalala nawo.”