Salimo 51:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, mogwirizana ndi chikondi chanu chokhulupirika.+ Fufutani zolakwa zanga mogwirizana ndi chifundo chanu chachikulu.+ Salimo 90:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mʼmawa, muzitisonyeza chikondi chanu chokhulupirika,+Kuti tizifuula mokondwera komanso kukhala mosangalala+ masiku onse a moyo wathu.
51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, mogwirizana ndi chikondi chanu chokhulupirika.+ Fufutani zolakwa zanga mogwirizana ndi chifundo chanu chachikulu.+
14 Mʼmawa, muzitisonyeza chikondi chanu chokhulupirika,+Kuti tizifuula mokondwera komanso kukhala mosangalala+ masiku onse a moyo wathu.