Salimo 103:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mofanana ndi bambo amene amasonyeza chifundo kwa ana ake,Yehova wasonyezanso chifundo kwa anthu amene amamuopa.+ Miyambo 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+Koma amene amawaulula nʼkuwasiya adzachitiridwa chifundo.+ Yesaya 43:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ineyo ndi amene ndikufafaniza zolakwa zako*+ chifukwa cha dzina langa,+Ndipo machimo ako sindidzawakumbukira.+ Yesaya 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ndipo zidzakhala ngati ndaziphimba ndi mtambo+Ndipo machimo ako adzakhala ngati ndawaphimba ndi mtambo waukulu. Bwerera kwa ine, ndipo ine ndidzakuwombola.+
13 Mofanana ndi bambo amene amasonyeza chifundo kwa ana ake,Yehova wasonyezanso chifundo kwa anthu amene amamuopa.+
13 Wobisa machimo ake zinthu sizidzamuyendera bwino,+Koma amene amawaulula nʼkuwasiya adzachitiridwa chifundo.+
25 Ineyo ndi amene ndikufafaniza zolakwa zako*+ chifukwa cha dzina langa,+Ndipo machimo ako sindidzawakumbukira.+
22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ndipo zidzakhala ngati ndaziphimba ndi mtambo+Ndipo machimo ako adzakhala ngati ndawaphimba ndi mtambo waukulu. Bwerera kwa ine, ndipo ine ndidzakuwombola.+