1 Mbiri 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ifetu ndife alendo pamaso panu, komanso okhala mʼdziko la eni ngati mmene analili makolo athu onse.+ Masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi+ ndipo ndife osakhalitsa. Yobu 14:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,Amakhala ndi moyo waufupi+ komanso wodzaza ndi mavuto.+ 2 Amaphuka ngati duwa kenako nʼkufota.+Amathawa ngati mthunzi ndipo saonekanso.+
15 Ifetu ndife alendo pamaso panu, komanso okhala mʼdziko la eni ngati mmene analili makolo athu onse.+ Masiku athu padziko lapansi ali ngati mthunzi+ ndipo ndife osakhalitsa.
14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,Amakhala ndi moyo waufupi+ komanso wodzaza ndi mavuto.+ 2 Amaphuka ngati duwa kenako nʼkufota.+Amathawa ngati mthunzi ndipo saonekanso.+