Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 33:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiye ngati mwandikomeradi mtima, chonde ndidziwitseni njira zanu+ kuti ndikudziweni komanso kuti mupitirize kundikomera mtima. Kumbukiraninso kuti mtundu uwu ndi anthu anu.”+

  • Salimo 86:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndilangizeni inu Yehova, za njira yanu.+

      Kuti ndiyende mʼchoonadi chanu.+

      Ndithandizeni kuti ndiziopa dzina lanu ndi mtima wonse.*+

  • Salimo 143:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Mʼmawa ndichititseni kumva za chikondi chanu chokhulupirika,

      Chifukwa ndimadalira inu.

      Ndidziwitseni njira imene ndikuyenera kuyendamo,+

      Chifukwa ndimadalira inu kuti muzinditsogolera.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena