Salimo 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Bwererani, inu Yehova, mudzandipulumutse.+Ndipulumutseni chifukwa cha chikondi chanu chokhulupirika.+ Salimo 51:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, mogwirizana ndi chikondi chanu chokhulupirika.+ Fufutani zolakwa zanga mogwirizana ndi chifundo chanu chachikulu.+
4 Bwererani, inu Yehova, mudzandipulumutse.+Ndipulumutseni chifukwa cha chikondi chanu chokhulupirika.+
51 Ndikomereni mtima inu Mulungu, mogwirizana ndi chikondi chanu chokhulupirika.+ Fufutani zolakwa zanga mogwirizana ndi chifundo chanu chachikulu.+