Salimo 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidziwitseni njira zanu, inu Yehova.+Ndiphunzitseni kuyenda mʼnjira zanu.+ Salimo 86:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndilangizeni inu Yehova, za njira yanu.+ Kuti ndiyende mʼchoonadi chanu.+ Ndithandizeni kuti ndiziopa dzina lanu ndi mtima wonse.*+ Yesaya 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngakhale kuti Yehova adzakupatsani mavuto kuti akhale chakudya chanu ndi kuponderezedwa kuti kukhale madzi anu akumwa,+ Mlangizi wanu wamkulu adzasiya kudzibisa ndipo maso anu adzaona Mlangizi wanu wamkulu.+ Yesaya 54:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana ako onse azidzaphunzitsidwa ndi Yehova,+Ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+
11 Ndilangizeni inu Yehova, za njira yanu.+ Kuti ndiyende mʼchoonadi chanu.+ Ndithandizeni kuti ndiziopa dzina lanu ndi mtima wonse.*+
20 Ngakhale kuti Yehova adzakupatsani mavuto kuti akhale chakudya chanu ndi kuponderezedwa kuti kukhale madzi anu akumwa,+ Mlangizi wanu wamkulu adzasiya kudzibisa ndipo maso anu adzaona Mlangizi wanu wamkulu.+