4 Ndidziwitseni njira zanu, inu Yehova.+
Ndiphunzitseni kuyenda mʼnjira zanu.+
ה [He]
5 Ndithandizeni kuti ndiziyenda mʼchoonadi chanu ndipo mundiphunzitse,+
Chifukwa inu ndinu Mulungu amene mumandipulumutsa.
ו [Waw]
Ndimayembekezera inu tsiku lonse.