Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 16:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa koma uli wachilungamo+

      Kusiyana nʼkupeza zinthu zambiri mopanda chilungamo.+

  • Miyambo 30:8, 9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Zinthu zabodza komanso mawu onama muziike kutali ndi ine.+

      Musandipatse umphawi kapena chuma.

      Mungondipatsa chakudya chokwanira,+

       9 Kuti ndisakhute kwambiri nʼkukukanani kuti: “Kodi Yehova ndi ndani?”+

      Ndiponso kuti ndisasauke nʼkukaba ndi kuchititsa kuti dzina la Mulungu wanga linyozedwe.

  • 1 Timoteyo 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Nʼzoona kuti kukhala wodzipereka kwa Mulungu+ komanso kukhala wokhutira ndi zimene tili nazo, ndi njira yopezera phindu lalikulu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena