Salimo 90:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mapiri asanabadwe,Kapena musanakhazikitse dziko lapansi komanso nthaka,+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+ Danieli 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndinapitiriza kuona masomphenya usikuwo ndipo ndinaona winawake wooneka ngati mwana wa munthu+ akubwera mʼmitambo. Iye analoledwa kufika kwa Wamasiku Ambiri+ uja ndipo anamubweretsa pafupi kwambiri ndi Wamasiku Ambiriyo. Danieli 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 mpaka pamene Wamasiku Ambiri+ anabwera ndipo anapereka chiweruzo chokomera oyera a Mulungu Wamkulu.+ Ndipo nthawi yomwe inaikidwiratu yoti oyerawo atenge ufumu inakwana.+ Habakuku 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Yehova, mwakhala mulipo kuyambira kalekale.+ Inu Mulungu wanga, Mulungu wanga Woyera, inu simufa.*+ Inu Yehova, mwasankha Akasidi kuti apereke chiweruzo chanu.Inu Thanthwe langa,+ mwawasankha kuti mupereke chilango.*+
2 Mapiri asanabadwe,Kapena musanakhazikitse dziko lapansi komanso nthaka,+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+
13 Ndinapitiriza kuona masomphenya usikuwo ndipo ndinaona winawake wooneka ngati mwana wa munthu+ akubwera mʼmitambo. Iye analoledwa kufika kwa Wamasiku Ambiri+ uja ndipo anamubweretsa pafupi kwambiri ndi Wamasiku Ambiriyo.
22 mpaka pamene Wamasiku Ambiri+ anabwera ndipo anapereka chiweruzo chokomera oyera a Mulungu Wamkulu.+ Ndipo nthawi yomwe inaikidwiratu yoti oyerawo atenge ufumu inakwana.+
12 Inu Yehova, mwakhala mulipo kuyambira kalekale.+ Inu Mulungu wanga, Mulungu wanga Woyera, inu simufa.*+ Inu Yehova, mwasankha Akasidi kuti apereke chiweruzo chanu.Inu Thanthwe langa,+ mwawasankha kuti mupereke chilango.*+