Levitiko 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aliyense wa inu azilemekeza* mayi ndi bambo ake,+ ndipo muzisunga masabata anga.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu. Miyambo 31:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Amatsegula pakamwa pake mwanzeru,+Ndipo lamulo la kukoma mtima lili* palilime lake. 2 Timoteyo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa ndikukumbukira chikhulupiriro chako chopanda chinyengo,+ chimene anayamba kukhala nacho ndi agogo ako aakazi a Loisi komanso amayi ako a Yunike, ndipo ndikukhulupirira kuti iwenso uli nacho.
3 Aliyense wa inu azilemekeza* mayi ndi bambo ake,+ ndipo muzisunga masabata anga.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
5 Chifukwa ndikukumbukira chikhulupiriro chako chopanda chinyengo,+ chimene anayamba kukhala nacho ndi agogo ako aakazi a Loisi komanso amayi ako a Yunike, ndipo ndikukhulupirira kuti iwenso uli nacho.