8 Kuposanso pamenepo, atakhala munthu, anadzichepetsa ndipo anakhala womvera mpaka imfa,+ inde imfa yapamtengo wozunzikirapo.+ 9 Pa chifukwa chimenechi, Mulungu anamukweza nʼkumupatsa udindo wapamwamba+ ndipo mokoma mtima anamupatsa dzina loposa lina lililonse.+