Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 65:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Iwo amanena kuti, ‘Khala kutali. Usandiyandikire,

      Chifukwa ndine woyera kwambiri kuposa iwe.’*

      Iwo ali ngati utsi mʼmphuno mwanga, ngati moto umene ukuyaka tsiku lonse.

  • Mateyu 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Samalani kuti musamachite zinthu zachilungamo pamaso pa anthu nʼcholinga choti akuoneni.+ Mukamachita zimenezi simudzalandira mphoto kwa Atate wanu amene ali kumwamba.

  • Aroma 10:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndipo chifukwa chosadziwa chilungamo cha Mulungu,+ iwo sanagonjere chilungamocho+ koma anafuna kukhazikitsa chawochawo.+

  • Aroma 14:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Nanga nʼchifukwa chiyani umaweruza mʼbale wako?+ Kapenanso nʼchifukwa chiyani umanyoza mʼbale wako? Popeza tonse tidzaima patsogolo pa mpando woweruzira wa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena