-
Mlaliki 5:15, 16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Monga mmene munthu anabadwira kuchokera mʼmimba mwa mayi ake, adzapitanso wamaliseche ngati mmene anabwerera.+ Ndipo sangatenge chilichonse pa ntchito yake imene anaigwira mwakhama.+
16 Palinso chinthu china chomvetsa chisoni kwambiri:* Monga mmene munthu anabwerera, adzapitanso chimodzimodzi. Ndipo kodi munthu amene amagwira ntchito mwakhama koma zonse nʼkungopita ndi mphepo amapindula chiyani?+
-