Salimo 15:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova, ndi ndani amene angakhale mlendo mutenti yanu? Ndi ndani amene angakhale mʼphiri lanu lopatulika?+ 2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,*+Amene amachita zinthu zabwino+Komanso kulankhula zoona mumtima mwake.+
15 Inu Yehova, ndi ndani amene angakhale mlendo mutenti yanu? Ndi ndani amene angakhale mʼphiri lanu lopatulika?+ 2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,*+Amene amachita zinthu zabwino+Komanso kulankhula zoona mumtima mwake.+