-
Yesaya 14:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Okuona adzakuyangʼana modabwa.
Adzakuyangʼanitsitsa nʼkunena kuti,
‘Kodi munthu amene ankagwedeza dziko lapansi uja ndi ameneyu,
Amene ankachititsa kuti maufumu anjenjemere,+
17 Amene anachititsa dziko lapansi kukhala ngati chipululu,
Nʼkugonjetsa mizinda yake,+
Amene sanalole kuti akaidi ake azipita kwawo?’+
-