Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Mose anatambasula dzanja lake nʼkuloza panyanja,+ ndipo Yehova anachititsa kuti mphepo yamphamvu yakumʼmawa igawe nyanjayo usiku wonse nʼkuumitsa pansi pake.+ Choncho madziwo anagawanika.+

  • Ekisodo 14:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Koma Aisiraeli anayenda panthaka youma pakati pa nyanja,+ ndipo madzi anaima ngati khoma kudzanja lawo lamanja ndi lamanzere.+

  • Salimo 106:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Iye analamula* ndipo Nyanja Yofiira inauma.

      Anatsogolera anthu ake kudutsa pakati pa madzi akuya ngati akudutsa mʼchipululu.+

  • Yesaya 51:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+

      Si iwe kodi amene unapangitsa kuti pansi pa nyanja pakhale njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena