Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 29:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pangotsala kanthawi kochepa kuti Lebanoni asanduke munda wa zipatso,+

      Ndipo munda wa zipatsowo udzangokhala ngati nkhalango.+

  • Yesaya 32:14, 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Chifukwa nsanja yokhala ndi mpanda wolimba yasiyidwa.

      Mzinda waphokoso wasiyidwa.+

      Ofeli+ ndi nsanja ya mlonda zasanduka chipululu mpaka kalekale.

      Zasanduka malo amene abulu amʼtchire akusangalalako,

      Komanso malo odyetserako ziweto,+

      15 Mpaka mzimu utatsanulidwa pa ife kuchokera kumwamba,+

      Ndiponso chipululu chitakhala munda wa zipatso,

      Komanso munda wa zipatsowo utayamba kuoneka ngati nkhalango.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena