Numeri 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzamuona, koma osati panopa;Ndidzamupenya, koma osati posachedwa. Nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu+ idzatuluka mu Isiraeli.+ Ndipo iye adzaphwanyadi chipumi cha Mowabu+Ndi mitu ya asilikali onse ankhanza. Amosi 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho ndidzatumiza moto ku Mowabu,Ndipo udzawotcheratu nsanja zolimba za Kerioti.+Mowabu adzafa pakati pa phokoso,Pakati pa mfuu yankhondo ndiponso kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa.+
17 Ndidzamuona, koma osati panopa;Ndidzamupenya, koma osati posachedwa. Nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu+ idzatuluka mu Isiraeli.+ Ndipo iye adzaphwanyadi chipumi cha Mowabu+Ndi mitu ya asilikali onse ankhanza.
2 Choncho ndidzatumiza moto ku Mowabu,Ndipo udzawotcheratu nsanja zolimba za Kerioti.+Mowabu adzafa pakati pa phokoso,Pakati pa mfuu yankhondo ndiponso kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa.+