Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 25:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mayina a ana a Isimaeli, malinga ndi mabanja awo ndi awa: Nebayoti,+ mwana woyamba wa Isimaeli, Kedara,+ Adibeele, Mibisamu,+

  • Yesaya 42:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chipululu ndi mizinda yake zifuule+

      Komanso midzi imene kumakhala Akedara.+

      Anthu amene amakhala mʼdera lamatanthwe afuule mosangalala.

      Anthuwo afuule kuchokera pamwamba pa mapiri.

  • Yesaya 60:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Nkhosa zonse za ku Kedara+ zidzasonkhanitsidwa kwa iwe.

      Nkhosa zamphongo za ku Nebayoti+ zidzakutumikira.

      Ine ndidzazilandira paguwa langa lansembe,+

      Ndipo ndidzakongoletsa nyumba yanga yaulemerero.*+

  • Ezekieli 27:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Unalemba ntchito Aluya ndi atsogoleri onse a ku Kedara,+ amene ankagulitsa ana a nkhosa, nkhosa zamphongo ndi mbuzi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena