-
Ezekieli 6:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Uwauze kuti, ‘Inu mapiri a Isiraeli, mvetserani zimene akunena Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa: Izi nʼzimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, akunena kwa mapiri, zitunda, mitsinje ndi zigwa: “Ine ndidzakubweretserani lupanga ndipo ndidzawononga malo anu okwezeka.
-