-
Yesaya 57:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Amene mukukhala ndi chilakolako champhamvu chogonana pakati pa mitengo ikuluikulu,+
Pansi pa mtengo uliwonse wa masamba ambiri?+
Kodi si inu amene mumapha ana mʼzigwa,*+
Pakati pa matanthwe?
6 Gawo lako lili pamodzi ndi miyala yosalala yamʼchigwa.*+
Inde, gawo lako ndi limeneli.
Ndipo umapereka nsembe zachakumwa, ndiponso mphatso kwa zinthu zimenezi.+
Kodi ine ndikhutire* ndi zinthu zimenezi?
-