Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Malaki 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Taonani! Ine ndikutumiza mthenga wanga ndipo adzandikonzera njira.+ Mwadzidzidzi, Ambuye woona, amene anthu inu mukumufunafuna, adzabwera kukachisi wake.+ Ndiponso mthenga wa pangano amene mukumuyembekezera mosangalala adzabwera. Iye adzabwera ndithu,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.

  • Mateyu 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mneneri Yesaya ananeneratu za iyeyu+ mʼmawu awa: “Winawake akufuula mʼchipululu kuti: ‘Konzani njira ya Yehova!* Muwongole misewu yake.’”+

  • Maliko 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼbuku la mneneri Yesaya kuti: “(Taona! Ine ndikutumiza mthenga wanga kuti atsogole* kukakukonzera njira.)*+

  • Luka 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Komanso adzatsogola monga kalambulabwalo wa Mulungu ali ndi mzimu ndi mphamvu ngati za Eliya.+ Iye adzatembenuza mitima ya abambo kuti ikhale ngati ya ana+ ndipo anthu osamvera adzawatembenuzira ku nzeru yeniyeni ya anthu olungama. Adzachita zimenezi kuti asonkhanitse anthu amene akonzekera kutumikira Yehova.”*+

  • Yohane 3:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Inunso ndinu mboni pa zimene ndinanena kuti, ‘Ine si Khristu,+ koma ndinatumizidwa monga kalambulabwalo wake.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena