Salimo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndifotokoza zimene Yehova wanena.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+ Mateyu 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Panamvekanso mawu ochokera kumwamba+ onena kuti: “Uyu ndi Mwana wanga+ wokondedwa ndipo amandisangalatsa kwambiri.”+ Luka 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ndipo mzimu woyera wooneka ngati nkhunda unatsika kudzamutera. Ndiyeno panamveka mawu ochokera kumwamba akuti: “Iwe ndi Mwana wanga wokondedwa, umandisangalatsa kwambiri.”+ 2 Petulo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa Khristu analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu, Atate wathu, pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu kuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa, amene amandisangalatsa kwambiri.”+
7 Ndifotokoza zimene Yehova wanena.Iye wandiuza kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga,+Lero, ine ndakhala bambo ako.+
17 Panamvekanso mawu ochokera kumwamba+ onena kuti: “Uyu ndi Mwana wanga+ wokondedwa ndipo amandisangalatsa kwambiri.”+
22 ndipo mzimu woyera wooneka ngati nkhunda unatsika kudzamutera. Ndiyeno panamveka mawu ochokera kumwamba akuti: “Iwe ndi Mwana wanga wokondedwa, umandisangalatsa kwambiri.”+
17 Chifukwa Khristu analandira ulemu ndi ulemerero kuchokera kwa Mulungu, Atate wathu, pamene mawu anamveka kwa iye kuchokera mu ulemerero waukulu kuti: “Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa, amene amandisangalatsa kwambiri.”+