Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aheberi 11:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Kodi ndiperekenso zitsanzo zina? Nthawi indichepera kuti ndipitirize kufotokoza za Gidiyoni,+ Baraki,+ Samisoni,+ Yefita,+ Davide+ komanso Samueli+ ndi aneneri ena.

  • Aheberi 11:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Anaponyedwa miyala,+ anayesedwa, anadulidwa pakati, anaphedwa ndi lupanga+ ndiponso anayendayenda atavala zikopa za nkhosa ndi zikopa za mbuzi.+ Ankasowa zinthu, ankazunzidwa+ komanso ankakumana ndi mavuto ena.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena