Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 7:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ufumu, ulamuliro, ndi ulemerero wa maufumu apadziko lonse lapansi zinaperekedwa kwa anthu amene ndi oyera a Mulungu Wamkulu.+ Ufumu wawo udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo maulamuliro onse adzawatumikira ndi kuwamvera.’

  • Luka 22:28-30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Komabe, inu ndi amene mwakhalabe ndi ine+ mʼmayesero anga.+ 29 Choncho ndikuchita nanu pangano, mofanana ndi mmene Atate wanga wachitira pangano la ufumu ndi ine,+ 30 kuti mukadye ndi kumwa patebulo langa mu Ufumu wanga,+ komanso kuti mukakhale mʼmipando yachifumu+ kuweruza mafuko 12 a Isiraeli.+

  • Aheberi 12:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Choncho, popeza kuti tidzalandira Ufumu umene sungagwedezeke, tiyeni tikhalebe okhulupirika kuti Mulungu apitirize kutisonyeza kukoma mtima kwakukulu, kuti tizichita utumiki wopatulika mʼnjira yovomerezeka, moopa Mulungu komanso mwaulemu kwambiri.

  • Yakobo 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Tamverani abale anga okondedwa. Kodi Mulungu sanasankhe anthu amene dzikoli limawaona kuti ndi osauka kuti akhale olemera mʼchikhulupiriro+ komanso kuti akhale oyenera kupatsidwa Ufumu umene Mulungu analonjeza anthu amene amamukonda?+

  • Chivumbulutso 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 nʼkutipanga kukhala mafumu+ ndi ansembe+ kuti titumikire Mulungu wake ndi Atate wake, kwa iyeyo kukhale ulemerero ndi mphamvu kwamuyaya. Ame.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena