-
Machitidwe 25:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Tsiku lotsatira, Agiripa ndi Berenike anabwera ndi ulemu waukulu wachifumu nʼkulowa mʼchipinda chimene anthu ankasonkhana. Anali ndi akuluakulu a asilikali komanso anthu otchuka amumzindawo ndipo Fesito atalamula, anabweretsa Paulo.
-