Luka 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho gulu lonse linanyamuka pamodzi nʼkupita ndi Yesu kwa Pilato.+ Machitidwe 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza Mtumiki wake+ Yesu,+ amene inu munamupereka+ ndiponso kumukana pamaso pa Pilato, ngakhale kuti Pilatoyo ankafuna kumumasula. Machitidwe 13:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa anthu a ku Yerusalemu ndi olamulira awo sanamuzindikire. Koma pamene ankamuweruza, anakwaniritsa zimene aneneri ananena,+ zomwe zimawerengedwa mokweza sabata lililonse. 28 Ngakhale kuti sanapeze chifukwa chomuphera,+ anaumiriza Pilato kuti ameneyu aphedwe.+
13 Mulungu wa Abulahamu, wa Isaki ndi wa Yakobo,+ Mulungu wa makolo athu, ndi amene walemekeza Mtumiki wake+ Yesu,+ amene inu munamupereka+ ndiponso kumukana pamaso pa Pilato, ngakhale kuti Pilatoyo ankafuna kumumasula.
27 Chifukwa anthu a ku Yerusalemu ndi olamulira awo sanamuzindikire. Koma pamene ankamuweruza, anakwaniritsa zimene aneneri ananena,+ zomwe zimawerengedwa mokweza sabata lililonse. 28 Ngakhale kuti sanapeze chifukwa chomuphera,+ anaumiriza Pilato kuti ameneyu aphedwe.+